*COD & Shipping Charges may apply on certain items.
Review final details at checkout.
₹1829
₹2373
22% OFF
Hardback
All inclusive*
Qty:
1
About The Book
Description
Author
Celesse the healer cat is a highly respected member of the neighborhood. As the mistresss favorite cat she spends lazy days in the warmth of the house. One snowy night a mother hare rushes in desperate for help. Reluctantly the healer cat travels with her through a nighttime snowstorm and biting cold winds. In a dark forest Celesse comes face-to-face with a scary surprise and is forced to gather her powers for the first time in a while. --- Mphaka winawake dzina lake Silese ankatha kuchiritsa matenda osiyanasiyana. Chifukwa cha mphatso yakeyi mphakayu ankalemekezedwa kwambiri mdera lonse limene amakhala. Nawonso adona a mnyumba imene Silese ankakhala ankamkonda kwambiri poyerekeza ndi ziweto zonse zimene anali nazo panyumbapo. Tsiku lina mwana wa kalulu anadwala mwakayakaya. Mayi wake ataona kukula kwa matendawo anapita kukapempha mphaka wochiritsa uja kuti abwere adzathandize mwanayo. Koma mphakayo sankafuna kumuthandiza chifukwa kunja kunali kutada komanso kukuzizira kwambiri. Kaluluyo ataumirirabe mphakayo analolera nkunyamuka. Ali mnjira anakumana ndi nkhandwe yoopsa kwambiri. Koma Silese anakwanitsa kulimbana nayo ndipo anapitiriza ulendo wawo. Kenako anafika kunyumba kwa kaluluyo ndipo anathandiza mwana wodwala uja. Kutacha mmawa dzuwa linatuluka ndipo kunja kunayamba kufunda. Silese anauyamba ulendo wobwerera kwawo ali ndi chimwemwe chodzadza tsaya.